+265 88 761 6554 info@edithkachalebanda.com
Cyclone Freddy House Donations
Edith
Jan 30, 2024
Mabanja asanu ndi awiri omwe amasowa pokhala potsatira ngozi yamadzi osefukira odza ndi namondwe wa Freddy m’boma la Phalombe, lero asamukira nyumba zodalilika zomwe bungwe la Malawi Red Cross Society (MRCS) lawangira.
M’modzi mwa akuluakulu ku MRCS, a Patrick Duncan Phiri, wati thandizo la K50 million lochoka kubungwe la Big Win kudzera ku Joyce Banda Foundation ndilo agwilitsa ntchito pomanga nyumbazi.
Mkati mwachimwemwe cha anthu omwe apindulawa, mkulu wa Joyce Banda Foundation, a Edith Akridge, wati apitilira kupeleka thandizo losiyana siyana pazosowa za anthuwa.
(by Alex Banda-Blantyre: 01/11/2024)

0 Comments

Submit a Comment

Your email address will not be published. Required fields are marked *

You may also like

Maize Donation From The Joyce Banda Foundation

Maize Donation From The Joyce Banda Foundation

Over five hundred families around Domasi in Zomba have today received free maize from the Joyce Banda Foundation. Speaking during the distribution, Edith Arkridge, managing director of the Foundation, said the magnitude of hunger in the area cannot be overemphasized....